Maskal – Samadziwa

Maskal Samadziwa

Maskal – Samadziwa Lyrics

Artist: Maskal
Song: Samadziwa

Oh, lala-lala, lala-lala
Oh, lalala, lala-lala-lala, lalala, oh
Ndinakumana naye anali yekha
Nthawi nkumapita tikumacheza

Pang’onopang’ono tikudziwana
Palibe amadziwa tidzafika pano
Mwa iwe ndinapeza mzanga
Mdenje la chikondi ndinagweramo

Unandipatsa mtima wako ndisunge
Chikhulupiliro unapeza mwa ineyo
Lero anthu ayamba kudziwa
Akuwona chikondi changa pa iweyo

Akuti iwe ndi ine ndife osiyana
Koma za chikondi changa (Samadziwa)
Za mtima mwanga (Samadziwa)
M’maganizo mwanga (Samadziwa)

Za nkhawa zanga (Samadziwa)
Komwe tachokela (Samadziwa)
Momwe tadutsa (Samadziwa)
Komwe tikupita (Samadziwa)

Za nkhawa zanga (Samadziwa), oh
Mchikondi chathu tinatsala tokha
Tinachisamalira lero chakula
Lero maluwa ayamba kuwoneka

Ena abwera aponyapo moto
Dzulo munabwera ndi chikwanje
Lero mwatiponyela minga
Khalidwe lanu la mtundu wanji?

Ndifunseko mumamva bwanji?
Mwatenga zoyipa zones
Kuvindikila chikondi chathu
Nkumati ndife osiyana

Za chikondi changa (Samadziwa)
Oh (Samadziwa)
Za mtima wanga (Samadziwa)
Maganizo wanga (Samadziwa)

Nkhawa zanga (Samadziwa)
Oh (Samadziwa)
Momwe tadutsa (Samadziwa)
Komwe tachokela (Samadziwa)

Oh, samadziwa, sangadziwe
Oh, lala-lalala, lala-lala
Za chikondi changa (Samadziwa)
Za mtima mwanga (Samadziwa)

Maganizo anga (Samadziwa)
Nkhawa zanga (Samadziwa)
Momwe tadutsa (Samadziwa)
Komwe tikupita (Samadziwa)

Oh (Samadziwa)
Eh (Samadziwa)
Sangadziwe (Samadziwa)
Samadziwa (Samadziwa)

Oh (Samadziwa)
(Samadziwa)
Samadziwa (Samadziwa)
Oh (Samadziwa)

(Samadziwa)
(Samadziwa)
Find more lyrics at https://dcslyrics.com

You can purchase their music thru
DCSLyrics.com Amazon Music    DCSLyrics.com Apple Music
Disclosure: As an Amazon Associate and an Apple Partner, we earn from qualifying purchases

Samadziwa Lyrics – English Translation

Oh, the lala-up, a lala-lala
Oh, sole, Lala-Lala-Lala, Floo, OH
I met her was alone
Time goes to visit

Slowly we know each other
No knows we will get here
In you found my friend
The linked hook up I fell in

You gave me your hearts and keep
Faith found in me
Today people are starting to know
He sees my love for you

Say you and I are different
But about my love (they don’t know)
Of my heart (didn’t know)
In my mind (don’t know)

About my concerns (didn’t know)
Where we left (did not know)
The way we have passed (did not know)
Where we go (don’t know)

About my concerns (did not know), oh
In our love we were left alone
We took care of today’s grown
Today the flowers begin to appear

Some have come to throw fire
Yesterday came with a knight
Today you have thrown thy thorns
What kind of behavior is your favorite?

What do I ask you to feel?
You’ve taken the worst all
To cover our love
Says we’re different

About my love (they don’t know)
Oh (didn’t know)
Of my heart (didn’t know)
My attitude (didn’t know)

My concerns (didn’t know)
Oh (didn’t know)
The way we have passed (did not know)
Where we left (did not know)

Oh, they don’t know, they can’t know
Oh, a bit-flash, a lala
About my love (they don’t know)
Of my heart (didn’t know)

My mind (they don’t know)
My concerns (didn’t know)
The way we have passed (did not know)
Where we go (don’t know)

Oh (didn’t know)
Eh (didn’t know)
Cannot know (don’t know)
Didn’t know (didn’t know)

Oh (didn’t know)
(Didn’t know)
Didn’t know (didn’t know)
Oh (didn’t know)

(Didn’t know)
(Didn’t know)
Find more lyrics at https://dcslyrics.com

Maskal Lyrics – Samadziwa

Please support our site by sharing it.
And please follow our site to get the latest lyrics for all your favourite songs.

Please support the artist and us by purchasing your favourite music thru our Amazon Music and Apple Music links 🙂

You can purchase their music thru
DCSLyrics.com Amazon Music    DCSLyrics.com Apple Music
Disclosure: As an Amazon Associate and an Apple Partner, we earn from qualifying purchases

Release Year: 2021