Kelvin Sings – Kuyambila Lero

Kelvin Sings Kuyambila Lero

Kelvin Sings – Kuyambila Lero Lyrics

Artist: Kelvin Sings
Song: Kuyambila Lero

Ndinafatsa kulingalira ine, baby
Nkhawa inandigwira ine, ine, ah
Mandalitso onsewa dziwa amasawutsa mtima wanga
Komwe kuli kokuya sikomwe ndinaponya mbedza yanga

Koma ndazindikira kuti kunja konseku palibe amene angandikonde ngati iwe
Kundivetsa ngati iwe
Nkona ndidza kwa iwe
Chikondichi ndi chako, chako, chako

Mtimawu ndi wako, wako, wako
Udziwe kuyambila lero, yeah
Udziwe kuyambila lero, yeah
Zonsezi ndi zako, zako, zako

Mtimawu ndi wako, wako, wako
Ukamagona usiku wa lero, yeah
Udziwe kuyambila lero
Eko mtima wanga utenge

Palibe amene angawusamale bwino
Chauta nkhawa zathu ansenze
Palibe wina angazichengete bwino
Nde kuli konse tikafika (Kafika)

Nyengo zathu zizasintha (Zasintha)
Koma ndiyambe nkupepesa
(Pepa darlie ndinaswa mtima wako)
Koma ndazindikira kuti kunja konseku kulibe amene angandikonde ngati iwe

Kundivetsa ngati iwe
Nkona ndidza kwa iwe
Chikondichi ndi chako, chako, chako
Mtimawu ndi wako, wako, wako

Udziwe kuyambila lero, yeah
Udziwe kuyambila lero, yeah
Zonsezi ndi zako, zako, zako
Mtimawu ndi wako, wako, wako

Ukamagona usiku wa lero, yeah
Udziwe kuyambila lero
Chikondichi ndi chako, baby iwe
Mtimawu ndi wako

Kuyambira lero
Kuyambira lero
Udziwe kuyambila lero
Chikondichi ndi chako, chako, chako

Mtimawu ndi wako, wako, wako
Udziwe kuyambila lero, yeah
Udziwe kuyambila lero, yeah
Zonsezi ndi zako, zako, zako

Mtimawu ndi wako, wako, wako
Ukamagona usiku wa lero, yeah
Udziwe kuyambila lero
Find more lyrics at https://dcslyrics.com

You can purchase their music thru
DCSLyrics.com Amazon Music    DCSLyrics.com Apple Music
Disclosure: As an Amazon Associate and an Apple Partner, we earn from qualifying purchases

Kuyambila Lero Lyrics – English Translation

I gently meek me, Baby
The anxiety touched me, I, Ah,
All these groceries know won’t raise my heart
Where it’s so sweet not that I dropped my hook

But I’ve noticed that all the outside no one can love me like you
Understanding me like you
I will see it to you
This love is your own, your, yours

The manner is your own, your, thine
Know the start today, yeah
Know the start today, yeah
All of this is your, your, your

The manner is your own, your, thine
When you lie on the night of today, Yeah
Know the start today
Wrenew my heart take it

No one can take care of good
Our Feast Our Assembly
No one else can be well behaved
Where is it all over when we get (kit)

Our season changes (changes)
But I’ll start my apologies
(Pepa Darlie I broke your heart)
But I’ve noticed that all the outside no one would love me like you

Understanding me like you
I will see it to you
This love is your own, your, yours
The manner is your own, your, thine

Know the start today, yeah
Know the start today, yeah
All of this is your, your, your
The manner is your own, your, thine

When you lie on the night of today, Yeah
Know the start today
This love is your own, Baby you
The heart is your

From today
From today
Know the start today
This love is your own, your, yours

The manner is your own, your, thine
Know the start today, yeah
Know the start today, yeah
All of this is your, your, your

The manner is your own, your, thine
When you lie on the night of today, Yeah
Know the start today
Find more lyrics at https://dcslyrics.com

Kelvin Sings Lyrics – Kuyambila Lero

Please support our site by sharing it.
And please follow our site to get the latest lyrics for all your favourite songs.

Please support the artist and us by purchasing your favourite music thru our Amazon Music and Apple Music links 🙂

You can purchase their music thru
DCSLyrics.com Amazon Music    DCSLyrics.com Apple Music
Disclosure: As an Amazon Associate and an Apple Partner, we earn from qualifying purchases

Release Year: 2021